Luka 7:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Atatero anayandikira nʼkugwira chithathacho ndipo amene ananyamulawo anangoima. Kenako iye ananena kuti: “Mnyamata iwe, ndikunena ndi iwe, dzuka!”+ Luka Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 7:14 Mungakhale Ndi Moyo Mpaka Kalekale, lesson 16 Yesu—Ndi Njira, tsa. 94 Nsanja ya Olonda,3/1/2008, tsa. 23
14 Atatero anayandikira nʼkugwira chithathacho ndipo amene ananyamulawo anangoima. Kenako iye ananena kuti: “Mnyamata iwe, ndikunena ndi iwe, dzuka!”+
7:14 Mungakhale Ndi Moyo Mpaka Kalekale, lesson 16 Yesu—Ndi Njira, tsa. 94 Nsanja ya Olonda,3/1/2008, tsa. 23