Luka 7:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Ataona zimenezi anthu onse anachita mantha ndipo anayamba kutamanda Mulungu kuti: “Mneneri wamkulu waonekera pakati pathu.”+ Ananenanso kuti, “Mulungu wakumbukira anthu ake.”+ Luka Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 7:16 Mungakhale Ndi Moyo Mpaka Kalekale, lesson 16 Yesu—Ndi Njira, tsa. 95
16 Ataona zimenezi anthu onse anachita mantha ndipo anayamba kutamanda Mulungu kuti: “Mneneri wamkulu waonekera pakati pathu.”+ Ananenanso kuti, “Mulungu wakumbukira anthu ake.”+