-
Luka 7:20Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
20 Atafika kwa iye amunawo ananena kuti: “Yohane Mʼbatizi watituma kudzakufunsani kuti: ‘Kodi Mesiya amene tikumuyembekezera uja ndi inu kapena tiyembekezere wina?’”
-