Luka 7:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Mu ola limenelo iye anachiritsa anthu ambiri amene ankavutika ndi matenda osiyanasiyana+ komanso amene ankadwala mwakayakaya ndi kutulutsa mizimu yoipa. Anathandizanso anthu ambiri amene anali ndi vuto losaona kuti ayambe kuona.
21 Mu ola limenelo iye anachiritsa anthu ambiri amene ankavutika ndi matenda osiyanasiyana+ komanso amene ankadwala mwakayakaya ndi kutulutsa mizimu yoipa. Anathandizanso anthu ambiri amene anali ndi vuto losaona kuti ayambe kuona.