-
Luka 7:32Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
32 Iwo ali ngati ana aangʼono amene akhala pansi mumsika nʼkumafuulirana kuti: ‘Tinakuimbirani chitoliro, koma simunavine. Tinalira mofuula, koma inu simunalire.’
-