-
Luka 7:36Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
36 Ndiyeno Mfarisi wina anaumiriza Yesu kuti akadye naye. Choncho anapita kunyumba ya Mfarisiyo ndipo anamupatsa chakudya.
-