-
Luka 7:38Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
38 Atafika anagwada kumapazi ake nʼkuyamba kulira, moti anayamba kunyowetsa mapaziwo ndi misozi, kwinaku akupukuta mapaziwo ndi tsitsi lamʼmutu mwake. Komanso anakisa mapazi akewo mwachikondi nʼkuwapaka mafuta onunkhirawo.
-