Luka 7:39 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 39 Mfarisi amene anamuitana uja ataona zimenezi, mumtima mwake ananena kuti: “Munthuyu akanakhala kuti ndi mneneridi, akanadziwa kuti mkazi amene akumugwirayu ndi ndani, ndiponso kuti ndi wotani. Akanadziwa kuti ndi wochimwa.”+
39 Mfarisi amene anamuitana uja ataona zimenezi, mumtima mwake ananena kuti: “Munthuyu akanakhala kuti ndi mneneridi, akanadziwa kuti mkazi amene akumugwirayu ndi ndani, ndiponso kuti ndi wotani. Akanadziwa kuti ndi wochimwa.”+