Luka 7:41 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 41 “Amuna awiri anatenga ngongole kwa munthu wina wokongoza ndalama. Mmodzi anatenga ngongole ya madinari* 500, koma winayo anatenga ngongole ya madinari 50. Luka Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 7:41 Nsanja ya Olonda,8/15/2010, tsa. 6
41 “Amuna awiri anatenga ngongole kwa munthu wina wokongoza ndalama. Mmodzi anatenga ngongole ya madinari* 500, koma winayo anatenga ngongole ya madinari 50.