-
Luka 7:44Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
44 Atatero anacheukira mayi uja nʼkuuza Simoni kuti: “Wamuona mayiyu? Ngakhale kuti ndalowa mʼnyumba yako, sunandipatse madzi otsukira mapazi anga. Koma mayiyu wanyowetsa mapazi anga ndi misozi yake nʼkuwapukuta ndi tsitsi lake.
-