Luka 7:49 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 49 Anthu onse amene anakhala naye patebulopo anayamba kudzifunsa mumtima mwawo kuti: “Kodi munthu ameneyu ndi ndani amene amathanso ngakhale kukhululukira machimo?”+
49 Anthu onse amene anakhala naye patebulopo anayamba kudzifunsa mumtima mwawo kuti: “Kodi munthu ameneyu ndi ndani amene amathanso ngakhale kukhululukira machimo?”+