Luka 8:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Chifukwa palibe chobisika chimene sichidzaululika. Ndipo zinthu zonse zosungidwa mwachinsinsi kwambiri zidzadziwika, sizidzabisika mpaka kalekale.+
17 Chifukwa palibe chobisika chimene sichidzaululika. Ndipo zinthu zonse zosungidwa mwachinsinsi kwambiri zidzadziwika, sizidzabisika mpaka kalekale.+