Luka 8:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Choncho muzimvetsera mwatcheru kwambiri. Chifukwa amene ali nazo, adzapatsidwa zochuluka,+ koma amene alibe, adzalandidwa ngakhalenso zimene akuganizira kuti ali nazo.”+ Luka Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 8:18 Nsanja ya Olonda,11/15/2007, ptsa. 26-306/1/2005, tsa. 21 Galamukani!,2/8/1994, tsa. 27
18 Choncho muzimvetsera mwatcheru kwambiri. Chifukwa amene ali nazo, adzapatsidwa zochuluka,+ koma amene alibe, adzalandidwa ngakhalenso zimene akuganizira kuti ali nazo.”+