Luka 8:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Munthuyo ataona Yesu, anafuula kwambiri nʼkudzigwetsa pansi pamaso pake. Kenako anafuula mwamphamvu kuti: “Kodi mukufuna chiyani kwa ine, Yesu, Mwana wa Mulungu Wamʼmwambamwamba? Chonde ndikukupemphani, musandizunze.”+ Luka Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 8:28 Nsanja ya Olonda,5/15/1987, tsa. 26
28 Munthuyo ataona Yesu, anafuula kwambiri nʼkudzigwetsa pansi pamaso pake. Kenako anafuula mwamphamvu kuti: “Kodi mukufuna chiyani kwa ine, Yesu, Mwana wa Mulungu Wamʼmwambamwamba? Chonde ndikukupemphani, musandizunze.”+