-
Luka 8:30Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
30 Yesu anamufunsa kuti: “Dzina lako ndi ndani?” Iye anayankha kuti: “Khamu,” chifukwa mwa iye munalowa ziwanda zambiri.
-