-
Luka 8:33Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
33 Zitatero ziwandazo zinatuluka mwa munthuyo nʼkukalowa munkhumbazo. Nkhumba zonsezo zinathamangira kuphedi nʼkulumphira mʼnyanja ndipo zinamira.
-