-
Luka 8:34Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
34 Koma abusa a ziwetozo ataona zimene zinachitikazo, anathawa nʼkukanena zimenezi mumzinda ndi mʼmidzi.