-
Luka 8:37Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
37 Kenako gulu lonse lochokera mʼmidzi yapafupi ya Agerasa linamupempha kuti achoke kwawoko, chifukwa linagwidwa ndi mantha aakulu. Zitatero iye anakwera ngalawa kuti azipita.
-