Luka 8:41 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 41 Kenako panafika munthu wina dzina lake Yairo. Munthu ameneyu anali mtsogoleri wa sunagoge. Ndiyeno anadzigwetsa pamapazi a Yesu nʼkuyamba kumuchonderera kuti apite kunyumba kwake.+
41 Kenako panafika munthu wina dzina lake Yairo. Munthu ameneyu anali mtsogoleri wa sunagoge. Ndiyeno anadzigwetsa pamapazi a Yesu nʼkuyamba kumuchonderera kuti apite kunyumba kwake.+