Luka 8:44 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 44 Mayiyu anatsatira Yesu kumbuyo nʼkugwira ulusi wopota wamʼmphepete mwa malaya ake akunja.+ Nthawi yomweyo magazi ake anasiya kutuluka.
44 Mayiyu anatsatira Yesu kumbuyo nʼkugwira ulusi wopota wamʼmphepete mwa malaya ake akunja.+ Nthawi yomweyo magazi ake anasiya kutuluka.