Luka 8:45 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 45 Ndiyeno Yesu anafunsa kuti: “Ndi ndani amene wandigwira?” Onse atakana, Petulo anati: “Mlangizi, simukuona kuti anthu onsewa akuzungulirani ndipo akukupanikizani?”+
45 Ndiyeno Yesu anafunsa kuti: “Ndi ndani amene wandigwira?” Onse atakana, Petulo anati: “Mlangizi, simukuona kuti anthu onsewa akuzungulirani ndipo akukupanikizani?”+