-
Luka 8:47Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
47 Mayiyo ataona kuti zimene wachitazo zadziwika, anapita kwa Yesu akunjenjemera ndipo anagwada nʼkuulula pamaso pa anthu onse chimene chinamuchititsa kuti amugwire, komanso mmene wachirira nthawi yomweyo.
-