Luka 8:55 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 55 Zitatero mzimu* wake+ unabwerera ndipo nthawi yomweyo anadzuka.+ Ndiyeno Yesu anawauza kuti amupatse chakudya mtsikanayo. Luka Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 8:55 Mungakhale Ndi Moyo Mpaka Kalekale, lesson 30
55 Zitatero mzimu* wake+ unabwerera ndipo nthawi yomweyo anadzuka.+ Ndiyeno Yesu anawauza kuti amupatse chakudya mtsikanayo.