Luka 9:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Kenako Yesu anasonkhanitsa atumwi 12 aja nʼkuwapatsa mphamvu ndi ulamuliro pa ziwanda zonse+ komanso kuti azitha kuchiritsa matenda.+ Luka Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 9:1 Nsanja ya Olonda,7/15/1987, ptsa. 26-27
9 Kenako Yesu anasonkhanitsa atumwi 12 aja nʼkuwapatsa mphamvu ndi ulamuliro pa ziwanda zonse+ komanso kuti azitha kuchiritsa matenda.+