Luka 9:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Koma ena ankanena kuti Eliya waonekera. Enanso ankanena kuti mmodzi wa aneneri akale wauka.+