Luka 9:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Ndiyeno Herode anati: “Yohane ndinamudula mutu.+ Nanga amene akuchita zomwe ndikumvazi ndi ndani?” Choncho ankafunitsitsa atamuona.+ Luka Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 9:9 Yesu—Ndi Njira, tsa. 126 Nsanja ya Olonda,8/15/1987, tsa. 30
9 Ndiyeno Herode anati: “Yohane ndinamudula mutu.+ Nanga amene akuchita zomwe ndikumvazi ndi ndani?” Choncho ankafunitsitsa atamuona.+