Luka 9:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Koma gulu la anthu linadziwa zimenezi moti linamutsatira. Yesu anawalandira bwino nʼkuyamba kuwauza za Ufumu wa Mulungu, ndipo anachiritsa amene ankafunika kuchiritsidwa.+ Luka Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 9:11 Nsanja ya Olonda,2/15/2000, tsa. 2111/1/1994, tsa. 14
11 Koma gulu la anthu linadziwa zimenezi moti linamutsatira. Yesu anawalandira bwino nʼkuyamba kuwauza za Ufumu wa Mulungu, ndipo anachiritsa amene ankafunika kuchiritsidwa.+