-
Luka 9:16Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
16 Kenako anatenga mitanda ya mkate 5 ndi nsomba ziwiri zija nʼkuyangʼana kumwamba ndipo anadalitsa chakudyacho. Atatero ananyemanyema mitanda ya mkateyo nʼkuipereka kwa ophunzira ake kuti aipereke kwa anthuwo.
-