Luka 9:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Choncho onse anadya nʼkukhuta, ndipo anatolera zotsala zodzaza madengu 12.+