Luka 9:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Iwo anamuyankha kuti: “Akumanena kuti Yohane Mʼbatizi, ena akumati Eliya, koma ena akumanena kuti mmodzi wa aneneri akale.”+ Luka Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 9:19 Yesu—Ndi Njira, tsa. 142 Nsanja ya Olonda,12/15/1987, tsa. 8
19 Iwo anamuyankha kuti: “Akumanena kuti Yohane Mʼbatizi, ena akumati Eliya, koma ena akumanena kuti mmodzi wa aneneri akale.”+