-
Luka 9:29Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
29 Pamene ankapemphera, maonekedwe a nkhope yake anasintha ndipo chovala chake chinaoneka choyera kwambiri ndi chonyezimira.
-