Luka 9:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 Apa nʼkuti Petulo ndi ena amene anali naye atatheratu ndi tulo. Koma tulo titawathera, anaona ulemerero wake+ ndiponso amuna awiri ataima naye. Luka Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 9:32 Yesu—Ndi Njira, tsa. 144 Tsanzirani, tsa. 193 Nsanja ya Olonda,1/1/2010, tsa. 271/1/1988, tsa. 8
32 Apa nʼkuti Petulo ndi ena amene anali naye atatheratu ndi tulo. Koma tulo titawathera, anaona ulemerero wake+ ndiponso amuna awiri ataima naye.
9:32 Yesu—Ndi Njira, tsa. 144 Tsanzirani, tsa. 193 Nsanja ya Olonda,1/1/2010, tsa. 271/1/1988, tsa. 8