-
Luka 9:33Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
33 Ndiyeno pamene amunawa ankasiyana naye, Petulo anauza Yesu kuti: “Mlangizi, zingakhale bwino ife titamakhala pano. Choncho timange matenti atatu pano, imodzi yanu, imodzi ya Mose ndi ina ya Eliya.” Koma iye sankazindikira zimene ankanena.
-