Luka 9:36 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 36 Pamene mawuwo ankamveka, anaona kuti Yesu ali yekha. Koma iwo anakhala chete ndipo sanauze aliyense mʼmasiku amenewo chilichonse pa zimene anaonazo.+
36 Pamene mawuwo ankamveka, anaona kuti Yesu ali yekha. Koma iwo anakhala chete ndipo sanauze aliyense mʼmasiku amenewo chilichonse pa zimene anaonazo.+