-
Luka 9:42Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
42 Koma ngakhale pamene ankamupititsa kwa iye, chiwandacho chinamugwetsa pansi nʼkumuchititsa kuti aphuphe mwamphamvu. Yesu anakalipira mzimu wonyansawo nʼkuchiritsa mnyamatayo ndipo anamupereka kwa bambo ake.
-