-
Luka 9:43Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
43 Anthu onse anadabwa ndi mphamvu zodabwitsa za Mulungu.
Anthuwo adakali odabwa ndi zonse zimene iye ankachita, Yesu anauza ophunzira ake kuti:
-