-
Luka 9:47Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
47 Yesu atazindikira zimene ankaganiza mumtima mwawo, anatenga mwana wamngʼono nʼkumuimika pambali pake.