Luka 9:54 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 54 Ophunzira ake, Yakobo ndi Yohane+ ataona zimenezi, ananena kuti: “Ambuye, kodi mukufuna tiwaitanire moto kuchokera kumwamba kuti uwanyeketse?”+ Luka Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 9:54 Nsanja ya Olonda (Yophunzira),6/2018, tsa. 11 Galamukani!,8/8/2003, tsa. 31
54 Ophunzira ake, Yakobo ndi Yohane+ ataona zimenezi, ananena kuti: “Ambuye, kodi mukufuna tiwaitanire moto kuchokera kumwamba kuti uwanyeketse?”+