Luka 9:60 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 60 Yesu anamuuza kuti: “Asiye akufa+ aike akufa awo, koma iwe pita ukalengeze zokhudza Ufumu wa Mulungu kulikonse.”+ Luka Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 9:60 Yesu—Ndi Njira, tsa. 155 Nsanja ya Olonda,3/15/1988, ptsa. 24-256/1/1987, ptsa. 15-16
60 Yesu anamuuza kuti: “Asiye akufa+ aike akufa awo, koma iwe pita ukalengeze zokhudza Ufumu wa Mulungu kulikonse.”+