-
Luka 10:6Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
6 Ndipo ngati pakhomopo pali munthu wokonda mtendere, mtendere wanu udzakhala pa iye. Koma ngati palibe, udzabwerera kwa inu.
-