Luka 10:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Iwenso Kaperenao, kodi mwina udzakwezedwa kumwamba? Ayi, koma udzatsikira ku Manda.* Luka Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 10:15 Nsanja ya Olonda,7/1/1989, ptsa. 16-176/1/1988, tsa. 30