Luka 10:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Amene akukumverani, akumveranso ine.+ Amene akunyalanyaza inu, akunyalanyazanso ine ndipo amene akunyalanyaza ine, akunyalanyazanso Mulungu amene anandituma.”+ Luka Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 10:16 Gulu, ptsa. 71-72
16 Amene akukumverani, akumveranso ine.+ Amene akunyalanyaza inu, akunyalanyazanso ine ndipo amene akunyalanyaza ine, akunyalanyazanso Mulungu amene anandituma.”+