Luka 10:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Taonani! Inetu ndakupatsani ulamuliro kuti muzitha kupondaponda njoka ndi zinkhanira. Komanso ndakupatsani ulamuliro kuti mugonjetse mphamvu zonse za mdani,+ ndipo palibe chimene chidzakuvulazeni. Luka Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 10:19 Yesu—Ndi Njira, ptsa. 170-171 Nsanja ya Olonda,7/1/1988, tsa. 17
19 Taonani! Inetu ndakupatsani ulamuliro kuti muzitha kupondaponda njoka ndi zinkhanira. Komanso ndakupatsani ulamuliro kuti mugonjetse mphamvu zonse za mdani,+ ndipo palibe chimene chidzakuvulazeni.