-
Luka 10:34Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
34 Choncho anafika pamene panali munthuyo ndipo anathira mafuta komanso vinyo mʼmabala ake nʼkuwamanga. Kenako anamukweza pabulu wake nʼkupita naye kunyumba ya alendo kumene anamusamalira.
-