Luka 10:35 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 35 Tsiku lotsatira anatulutsa madinari* awiri nʼkupereka kwa mwini nyumba ya alendoyo ndipo anamuuza kuti: ‘Musamalireni bwino, mukawononga ndalama zina zowonjezera, ndidzakubwezerani ndikadzabwera.’ Luka Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 10:35 Galamukani!,6/8/1990, tsa. 18 Nsanja ya Olonda,7/15/1988, tsa. 25
35 Tsiku lotsatira anatulutsa madinari* awiri nʼkupereka kwa mwini nyumba ya alendoyo ndipo anamuuza kuti: ‘Musamalireni bwino, mukawononga ndalama zina zowonjezera, ndidzakubwezerani ndikadzabwera.’