-
Luka 11:7Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
7 Koma mnzake ali mʼnyumbayo nʼkuyankha kuti: ‘Usandivutitse ine. Takhoma kale chitseko, ndipo ine ndi ana anga tagona kale. Sindingathe kudzuka kuti ndikupatse kanthu.’
-