Luka 11:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Choncho ndikukuuzani, pitirizani kupempha+ ndipo adzakupatsani. Pitirizani kufunafuna ndipo mudzapeza. Pitirizani kugogoda ndipo adzakutsegulirani.+ Luka Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 11:9 Nsanja ya Olonda,2/1/2009, tsa. 179/15/1992, tsa. 145/15/1990, tsa. 14
9 Choncho ndikukuuzani, pitirizani kupempha+ ndipo adzakupatsani. Pitirizani kufunafuna ndipo mudzapeza. Pitirizani kugogoda ndipo adzakutsegulirani.+