Luka 11:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Kenako anatulutsa chiwanda mwa munthu chimene chinkamulepheretsa kulankhula.+ Chiwandacho chitatuluka, munthu wosalankhulayo analankhula ndipo gulu la anthu linadabwa kwambiri.+ Luka Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 11:14 Nsanja ya Olonda,8/15/1988, tsa. 8
14 Kenako anatulutsa chiwanda mwa munthu chimene chinkamulepheretsa kulankhula.+ Chiwandacho chitatuluka, munthu wosalankhulayo analankhula ndipo gulu la anthu linadabwa kwambiri.+