Luka 11:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Atadziwa maganizo awo,+ iye anawauza kuti: “Ufumu uliwonse wogawanika umatha ndipo nyumba yogawanika imagwa.
17 Atadziwa maganizo awo,+ iye anawauza kuti: “Ufumu uliwonse wogawanika umatha ndipo nyumba yogawanika imagwa.