-
Luka 11:18Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
18 Mofanana ndi zimenezi, ngati Satana nayenso wagawanika, kodi ufumu wake ungakhalepo bwanji? Chifukwa inu mukunena kuti ndimatulutsa ziwanda ndi mphamvu ya Belezebule.
-